Tito 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma iwe, lankhula zimene ziyenera ciphunzitso colamitsa:

2. okalamba akhale odzisunga, olemekezeka, odziletsa, olama m'cikhulupiriro, m'cikondi, m'cipiriro.

Tito 2