Numeri 6:25-27 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Yehova awalitse nkhope yace pa iwe, nakucitire cisomo; Yehova akweze nkhope yace pa iwe, nakupatse mtendere.