Numeri 27:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Ndipo unene ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Akafa munthu wamwamuna wopanda mwana wamwamuna, colowa cace acilandire mwana wace wamkazi.

9. Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ace colowa cace.

10. Ndipo akapanda kukhala nao abale, mupatse abale a atate wace colowa cace.

Numeri 27