Numeri 27:22-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Ndipo Mose anacita monga Yehova adamuuza; natenga Yoswa namuimitsa pamaso pa Eleazara wansembe, ndi pamaso pa khamu lonse;

23. namuikira manja ace, namlangiza monga Yehova adanena ndi dzanja la Mose.

Numeri 27