2 Timoteo 2:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo iwe, mwana wanga, limbika m'cisomo ca m'Kristu Yesu.

2. Ndipo zimene wazimva kwa ine mwa mboni zambiri, zomwezi uikize kwa anthu okhulupirika, amene adzadziwa kuphunzitsa enanso.

2 Timoteo 2